Miyambo 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Usakhale pakati pa anthu omwa vinyo kwambiri,+ ndiponso pakati pa anthu odya nyama mosusuka.+