1 Timoteyo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho woyang’anira akhale wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire,+ woganiza bwino,+ wadongosolo,+ wochereza alendo,+ ndiponso wotha kuphunzitsa.+ Tito 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mkulu ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi+ mmodzi, wa ana okhulupirira ndi osanenezedwa kuti ndi amakhalidwe oipa kapena osalamulirika.+
2 Choncho woyang’anira akhale wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire,+ woganiza bwino,+ wadongosolo,+ wochereza alendo,+ ndiponso wotha kuphunzitsa.+
6 Mkulu ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera,+ mwamuna wa mkazi+ mmodzi, wa ana okhulupirira ndi osanenezedwa kuti ndi amakhalidwe oipa kapena osalamulirika.+