1 Timoteyo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+ 2 Petulo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choyamba, inu mukudziwa kuti m’masiku otsiriza+ kudzakhala onyodola+ amene azidzatsatira zilakolako zawo,+
4 Komabe, mawu ouziridwa amanenadi kuti m’nthawi zam’tsogolo,+ ena adzagwa+ pa chikhulupiriro, chifukwa chomvetsera mawu ouziridwa omwe ndi osocheretsa,+ ndiponso ziphunzitso za ziwanda.+
3 Choyamba, inu mukudziwa kuti m’masiku otsiriza+ kudzakhala onyodola+ amene azidzatsatira zilakolako zawo,+