1 Petulo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 inunso monga miyala yamoyo mukumangidwa n’kukhala nyumba yauzimu+ kuti mudzakhale ansembe oyera, n’cholinga chakuti mupereke nsembe zauzimu+ zovomerezeka pamaso pa Mulungu kudzera mwa Yesu Khristu.+ Chivumbulutso 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo munawasandutsa mafumu+ ndi ansembe+ a Mulungu wathu,+ moti adzakhala mafumu+ olamulira dziko lapansi.” Chivumbulutso 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+
5 inunso monga miyala yamoyo mukumangidwa n’kukhala nyumba yauzimu+ kuti mudzakhale ansembe oyera, n’cholinga chakuti mupereke nsembe zauzimu+ zovomerezeka pamaso pa Mulungu kudzera mwa Yesu Khristu.+
10 Ndipo munawasandutsa mafumu+ ndi ansembe+ a Mulungu wathu,+ moti adzakhala mafumu+ olamulira dziko lapansi.”
6 Wodala+ ndi woyera+ ndiye aliyense wouka nawo pa kuuka koyamba. Pa iwo, imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi naye zaka 1,000.+