28 Ndiye chifukwa chake, poona kuti tidzalandira ufumu umene sungagwedezeke,+ tiyeni tipitirize kulandira kukoma mtima kwakukulu, kuti kudzera m’kukoma mtima kwakukulu kumeneko, tichitire Mulungu utumiki wopatulika m’njira yovomerezeka, ndipo tiuchite moopa Mulungu komanso mwaulemu waukulu.+