1 Mafumu 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Makoma a mkati mwa nyumbayo anawamanga ndi matabwa akuluakulu a mkungudza. Mkati mwa nyumbayo, kuchokera pansi mpaka kudenga anakutamo ndi matabwa. Komanso pansi pa nyumbayo anaikapo matabwa akuluakulu a mitengo ya junipa.*+ 1 Mafumu 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nyumba yonseyo anaikuta ndi golide mpaka kuimaliza, ndipo guwa lansembe lonse, lomwe linali pafupi ndi chipinda chamkati, analikuta ndi golide.+
15 Makoma a mkati mwa nyumbayo anawamanga ndi matabwa akuluakulu a mkungudza. Mkati mwa nyumbayo, kuchokera pansi mpaka kudenga anakutamo ndi matabwa. Komanso pansi pa nyumbayo anaikapo matabwa akuluakulu a mitengo ya junipa.*+
22 Nyumba yonseyo anaikuta ndi golide mpaka kuimaliza, ndipo guwa lansembe lonse, lomwe linali pafupi ndi chipinda chamkati, analikuta ndi golide.+