Zamkatimu
June 15, 2011
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
August 1-7, 2011
Pali Uthenga Wabwino Wofunika Kuti Anthu Onse Amve
TSAMBA 7
August 8-14, 2011
Mulungu Akuonetsa Chikondi Chake kwa Ife
TSAMBA 11
August 15-21, 2011
“Wetani Gulu la Nkhosa za Mulungu Lomwe Analisiya M’manja Mwanu”
TSAMBA 20
August 22-28, 2011
“Muzilemekeza Anthu Amene Akugwira Ntchito Mwakhama Pakati Panu”
TSAMBA 24
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 TSAMBA 7-15
M’buku la Aroma, mtumwi Paulo ananena za mbali ina ya “uthenga wabwino” imene imakhudza kwambiri anthu ochimwa. Kodi mbaliyi ndi iti ndipo mungapindule nayo bwanji? Nkhani ziwirizi zikuthandizani kumvetsa bwino ndiponso kuyamikira kwambiri nsembe ya Yesu komanso chikondi chimene Mulungu anasonyeza poipereka.
NKHANI ZOPHUNZIRA 3, 4 TSAMBA 20-28
Nkhani zimenezi zikufotokoza zimene akulu angachite posonyeza kuyamikira mwayi wawo woweta nkhosa. Zikufotokozanso mmene mpingo ungalemekezere akulu.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
3 Kodi Achinyamata Ayenera Kubatizidwa?
16 Kodi Abulahamu Analidi ndi Ngamila?
18 ‘Unditengerekonso Mipukutu, Makamaka Yazikopa Ija’
29 Kodi Mungatani Kuti Mukhale ndi “Moyo Wopambana”?