Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zabwino zimene munthu wolungama ankachita zikakumbukiridwa* amadalitsidwa,+Koma dzina la anthu oipa lidzawola.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:7 Nsanja ya Olonda,7/15/2001, tsa. 25-26
7 Zabwino zimene munthu wolungama ankachita zikakumbukiridwa* amadalitsidwa,+Koma dzina la anthu oipa lidzawola.+