Yesaya 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu anthu anga, ndimvereni.Iwe mtundu wanga,+ tchera khutu kwa ine. Chifukwa kwa ine kudzachokera lamulo+Ndipo ndidzachititsa kuti chilungamo changa chikhazikike ngati kuwala ku mitundu ya anthu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:4 Yesaya 2, tsa. 169
4 Inu anthu anga, ndimvereni.Iwe mtundu wanga,+ tchera khutu kwa ine. Chifukwa kwa ine kudzachokera lamulo+Ndipo ndidzachititsa kuti chilungamo changa chikhazikike ngati kuwala ku mitundu ya anthu.+