Yoweli 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Valani ziguduli ndipo lirani* inu ansembe.Lirani mofuula, inu atumiki apaguwa lansembe.+ Lowani, valani ziguduli usiku wonse inu atumiki a Mulungu wanga,Chifukwa nsembe yambewu+ ndi nsembe yachakumwa+ sizikubweranso mʼnyumba ya Mulungu wanu. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, tsa. 10
13 Valani ziguduli ndipo lirani* inu ansembe.Lirani mofuula, inu atumiki apaguwa lansembe.+ Lowani, valani ziguduli usiku wonse inu atumiki a Mulungu wanga,Chifukwa nsembe yambewu+ ndi nsembe yachakumwa+ sizikubweranso mʼnyumba ya Mulungu wanu.