Luka 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti kwenikweni, ndipo chizindikiro chosonyeza kuti nthawi yoti zinthu zimenezi zichitike yatsala pangʼono chidzakhala chiyani?”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 256 Nsanja ya Olonda,5/1/1999, tsa. 8-9
7 Ndiyeno anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti kwenikweni, ndipo chizindikiro chosonyeza kuti nthawi yoti zinthu zimenezi zichitike yatsala pangʼono chidzakhala chiyani?”+