Machitidwe 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo anakwiya chifukwa atumwiwo ankaphunzitsa anthu ndiponso kulalikira mosapita mʼmbali zoti Yesu anaukitsidwa.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:2 Kuchitira Umboni, tsa. 31
2 Iwo anakwiya chifukwa atumwiwo ankaphunzitsa anthu ndiponso kulalikira mosapita mʼmbali zoti Yesu anaukitsidwa.+