Machitidwe 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ataona kuti Petulo ndi Yohane akulankhula molimba mtima komanso atakumbukira kuti anali osaphunzira* ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anazindikira kuti ankayenda ndi Yesu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:13 Nsanja ya Olonda,9/1/2008, tsa. 155/15/2008, tsa. 30-315/1/2006, tsa. 22-23 Galamukani!,3/8/1998, tsa. 26
13 Ataona kuti Petulo ndi Yohane akulankhula molimba mtima komanso atakumbukira kuti anali osaphunzira* ndiponso anthu wamba,+ anadabwa kwambiri. Ndipo anazindikira kuti ankayenda ndi Yesu.+
4:13 Nsanja ya Olonda,9/1/2008, tsa. 155/15/2008, tsa. 30-315/1/2006, tsa. 22-23 Galamukani!,3/8/1998, tsa. 26