Machitidwe 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atamupeza anabwera naye ku Antiokeya. Iwo anasonkhana ndi mpingo kumeneko kwa chaka chathunthu ndipo anaphunzitsa anthu ambiri. Ku Antiokeya nʼkumene ophunzirawo anayamba kutchedwa Akhristu, motsogoleredwa ndi Mulungu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:26 Kuchitira Umboni, tsa. 74-76 Nsanja ya Olonda,7/15/2000, tsa. 25-266/1/1990, tsa. 19
26 Atamupeza anabwera naye ku Antiokeya. Iwo anasonkhana ndi mpingo kumeneko kwa chaka chathunthu ndipo anaphunzitsa anthu ambiri. Ku Antiokeya nʼkumene ophunzirawo anayamba kutchedwa Akhristu, motsogoleredwa ndi Mulungu.+