LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 103
  • “Kunyumba Ndi Nyumba”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Kunyumba Ndi Nyumba”
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • “Ku Nyumba ndi Nyumba”
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Imbirani Yehova
sn nyimbo 103

Nyimbo 103

“Kunyumba Ndi Nyumba”

(Machitidwe 20:20)

1. Kunyumba ndi nyumba

Ife timalalikira.

Konsekonse nkhosa za M’lungu

Zikudyetsedwa.

Zoti Ufumu wa M’lungu

Ukulamulira,

Akhristu akufalitsa,

Akulu ndi ana.

2. Khomo ndi khomo

Tinene za chipulumutso,

Dzina la M’lungu aitane,

Apeze moyo.

Adzaitana bwanji

Dzina lomwe sadziwa?

Choncho mumakomo awo

Tidzalilengeza.

3. Khomo ndi khomo

Tiyeni tifalitse mawu.

Asankhe okha kumvera

Kapena kukana.

Koma dzina la Yehova

Tidzalengezabe.

Ndipo potero

Tidzapezadi nkhosa zake.

(Onaninso Mac. 2:21; Aroma 10:14.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2022)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani