LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 115
  • Khalani ndi Moyo Wopambana

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khalani ndi Moyo Wopambana
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Moyo Ndi Wodabwitsa
    Imbirani Yehova
  • Moyo ni Cozizwitsa
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Umoyo wa Mpainiya
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Aphunzitseni Kucilimika
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 115

Nyimbo 115

Khalani ndi Moyo Wopambana

(Yoswa 1:8)

1. Mawu a Yehova M’lungu

Tiwerenge tonse

Ndipo tiwasinkhesinkhe

Tsiku lililonse.

Iwo atitsogolere

M’zomwe timachita,

(KOLASI)

Ukawerenga n’kumvera

Udzadalitsidwa.

Yenda ndi M’lungu upeze

Njira yopambana.

2. Mafumu mu Is’raeli

Analamulidwa:

‘Chilamulo cha Mulungu

Adzilemberetu.

Ndipo tsiku lililonse

Azichiwerenga.’

(KOLASI)

Ukawerenga n’kumvera

Udzadalitsidwa.

Yenda ndi M’lungu upeze

Njira yopambana.

3. Tikamaphunzira Mawu

Tsiku lililonse

Tikhala n’chiyembekezo

Komanso mtendere.

Tidzapita patsogolo

Tikasinkhasinkha.

(KOLASI)

Ukawerenga n’kumvera

Udzadalitsidwa.

Yenda ndi M’lungu upeze

Njira yopambana.

(Onaninso Deut. 17:18; 1 Maf. 2:3, 4; Sal. 119:1; Yer. 7:23.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2022)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani