LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 95
  • Kuwala Kuwonjezeleka

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kuwala Kuwonjezeleka
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Kuwala Kukuwonjezereka
    Imbirani Yehova
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 95

NYIMBO 95

Kuwala Kuwonjezeleka

Yopulinta

(Miyambo 14:18)

  1. 1. Aneneli anali kuphunzila,

    Za kubwela kwa Yesu Khristu.

    Mzimu woyela unaŵadziŵitsa,

    Kuti adzatipulumutsa.

    Umboni ukuonekela bwino,

    Kuti akulamulila.

    Kudziŵa zimenezi ni mwayidi

    Umene ise tapatsiwa.

    (KOLASI)

    Taleka kuyenda mumdima,

    Lomba tiyenda m’kuwala.

    Yehova atitsogolela;

    Ndipo amatiphunzitsa.

  2. 2. Yesu amatidyetsa mwauzimu,

    Mwa kapolo wake padziko.

    Kagulu aka kamatithandiza

    Kuti timvetsetse co’nadi.

    Tsopano zimene timaphunzila

    Zimatifika pamtima.

    Tiyamikila Yehova cifukwa

    Watiphunzitsa coonadi.

    (KOLASI)

    Taleka kuyenda mumdima,

    Lomba tiyenda m’kuwala.

    Yehova atitsogolela;

    Ndipo amatiphunzitsa.

(Onaninso Aroma 8:22; 1 Akor. 2:10; 1 Pet. 1:12.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2022)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani