LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 97
  • Moyo Umadalila Mau a Mulungu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Moyo Umadalila Mau a Mulungu
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Munadyapo Mkate Wamoyo?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2014
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 97

NYIMBO 97

Moyo Umadalila Mau a Mulungu

Yopulinta

(Mateyu 4:4)

  1. 1. Moyo wathu ‘madalila

    Mau a Yehova.

    Zonse iye ananena

    Zitipindulitsa.

    Timakhala na mtendele,

    Timadalitsidwa.

    (KOLASI)

    Moyo umadaliladi;

    Mau a Mulungu.

    Ngati ‘se tiwatsatila;

    Tidzadalitsidwa.

  2. 2. M’Mau a Mulungu wathu

    Tipeza zitsanzo,

    Za amuna ndi akazi,

    Okhulupilika.

    Tikaŵelenga za iwo

    Tilimbikitsidwa.

    (KOLASI)

    Moyo umadaliladi;

    Mau a Mulungu.

    Ngati ‘se tiwatsatila;

    Tidzadalitsidwa.

  3. 3. Mwa Mau ake Yehova

    Amatithandiza.

    Kukhala anthu olimba

    Olo tivutike.

    Mayeselo akabwela

    Amatitonthoza.

    (KOLASI)

    Moyo umadaliladi;

    Mau a Mulungu.

    Ngati ‘se tiwatsatila;

    Tidzadalitsidwa.

(Onaninso Yos. 1:8; Aroma 15:4.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2022)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani