Yophunzila
MARCH 2020
NKHANI ZOPHUNZILA: MAY 4-31, 2020
© 2019 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu. Kuti mupange copeleka, pitani pa copeleka.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’magazini ino tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
CITHUNZI CA PA CIKUTO:
Pamene Yesu anali na atumwi ake madzulo akuti maŵa adzaphedwa, anagogomeza za kufunika kwa cikondi (Onani nkhani yophunzila 13, ndime 1-2)