Mawu Amunsi
M’Mawu a Mulungu muli mfundo zimene zingatithandize kudziŵa nthawi yoyenela kukamba na nthawi yokhala cete. Tikadziŵa mfundo zimenezo na kuziseŵenzetsa, zokamba zathu zidzakhala zokondweletsa Yehova.