Genesis 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Masiku onse amene dziko lapansi lidzakhalapo, kubzala mbewu ndi kukolola sikudzatha. Ndiponso, nyengo yozizira ndi yotentha, chilimwe ndi chisanu, usana ndi usiku, zidzakhalapobe.”+
22 Masiku onse amene dziko lapansi lidzakhalapo, kubzala mbewu ndi kukolola sikudzatha. Ndiponso, nyengo yozizira ndi yotentha, chilimwe ndi chisanu, usana ndi usiku, zidzakhalapobe.”+