Genesis 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Farao ataona zimenezi anaitana Abulamu, n’kumufunsa kuti: “N’chiyani wandichitachi? N’chifukwa chiyani sunandiuze kuti ndi mkazi wako?+
18 Farao ataona zimenezi anaitana Abulamu, n’kumufunsa kuti: “N’chiyani wandichitachi? N’chifukwa chiyani sunandiuze kuti ndi mkazi wako?+