Miyambo 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wolungama akamanjenjemera pamaso pa munthu woipa, amakhala ngati kasupe woipitsidwa ndiponso chitsime chowonongedwa.+
26 Munthu wolungama akamanjenjemera pamaso pa munthu woipa, amakhala ngati kasupe woipitsidwa ndiponso chitsime chowonongedwa.+