Genesis 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumeneko, Isaki anafukulanso zitsime za madzi zimene zinakumbidwa m’masiku a Abulahamu bambo ake. Afilisiti anafotsera zitsimezo Abulahamu atamwalira,+ ndipo iye anazitchanso mayina amene bambo ake anazipatsa.+
18 Kumeneko, Isaki anafukulanso zitsime za madzi zimene zinakumbidwa m’masiku a Abulahamu bambo ake. Afilisiti anafotsera zitsimezo Abulahamu atamwalira,+ ndipo iye anazitchanso mayina amene bambo ake anazipatsa.+