Genesis 25:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Isaki anali kukonda kwambiri Esau chifukwa anali kum’phera nyama, koma Rabeka anali kukonda kwambiri Yakobo.+
28 Isaki anali kukonda kwambiri Esau chifukwa anali kum’phera nyama, koma Rabeka anali kukonda kwambiri Yakobo.+