Genesis 24:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Rabeka anali ndi mlongo wake dzina lake Labani.+ Ndipo Labani anathamanga kupita kwa munthu uja, yemwe anali kuchitsime, kunja kwa mzinda.
29 Rabeka anali ndi mlongo wake dzina lake Labani.+ Ndipo Labani anathamanga kupita kwa munthu uja, yemwe anali kuchitsime, kunja kwa mzinda.