Genesis 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anagula malo ndipo anamangapo msasa. Anawagula ndi ndalama zasiliva 100, kwa ana a Hamori, bambo wake wa Sekemu.+ Genesis 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Sekemu anaona mtsikanayu. Sekemuyu anali mwana wamwamuna wa Hamori, Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri a m’dzikolo. Atamuona, anamutenga n’kumugwiririra.+
19 Kenako anagula malo ndipo anamangapo msasa. Anawagula ndi ndalama zasiliva 100, kwa ana a Hamori, bambo wake wa Sekemu.+
2 Kenako Sekemu anaona mtsikanayu. Sekemuyu anali mwana wamwamuna wa Hamori, Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri a m’dzikolo. Atamuona, anamutenga n’kumugwiririra.+