Yoswa 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Tsopano chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu,+ ndipo tembenuzirani mitima yanu kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.” 1 Yohane 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu ana okondedwa, pewani mafano.+
23 “Tsopano chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu,+ ndipo tembenuzirani mitima yanu kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.”