Miyambo 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+ Luka 12:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndithu ndikukuuzani, Adzamuika kukhala woyang’anira zinthu zake zonse.+ 1 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+
35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+