Nehemiya 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno tsiku lina m’mwezi wa Nisani,*+ m’chaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inali kufuna vinyo. Pamenepo ine ndinatenga vinyoyo ndi kum’pereka kwa mfumu monga mwa nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake.+
2 Ndiyeno tsiku lina m’mwezi wa Nisani,*+ m’chaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inali kufuna vinyo. Pamenepo ine ndinatenga vinyoyo ndi kum’pereka kwa mfumu monga mwa nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake.+