Deuteronomo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Sankhani amuna anzeru, aluso+ ndi ozindikira+ m’mafuko anu, kuti ndiwaike kukhala atsogoleri anu.’+ 1 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+
13 Sankhani amuna anzeru, aluso+ ndi ozindikira+ m’mafuko anu, kuti ndiwaike kukhala atsogoleri anu.’+