Esitere 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mfumu inavula mphete yake yodindira+ imene inalanda Hamani ndi kuipereka kwa Moredekai. Pamenepo Esitere anaika Moredekai kuti ayang’anire nyumba ya Hamani.+ Salimo 75:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ndiye woweruza.+Amatsitsa wina ndi kukweza wina.+ Danieli 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+
2 Ndiyeno mfumu inavula mphete yake yodindira+ imene inalanda Hamani ndi kuipereka kwa Moredekai. Pamenepo Esitere anaika Moredekai kuti ayang’anire nyumba ya Hamani.+
29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+