Yeremiya 43:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye adzaphwanyaphwanya zipilala za ku Beti-semesi,* mzinda umene uli ku Iguputo. Ndipo nyumba za milungu ya Iguputo adzazitentha.”’” Ezekieli 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anyamata a ku Oni+ ndi ku Pibeseti adzaphedwa ndi lupanga. Anthu a m’mizinda imeneyi adzatengedwa kupita ku ukapolo.
13 Iye adzaphwanyaphwanya zipilala za ku Beti-semesi,* mzinda umene uli ku Iguputo. Ndipo nyumba za milungu ya Iguputo adzazitentha.”’”
17 Anyamata a ku Oni+ ndi ku Pibeseti adzaphedwa ndi lupanga. Anthu a m’mizinda imeneyi adzatengedwa kupita ku ukapolo.