Genesis 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo abale akewo anamufunsa kuti: “Kodi iweyo ndithu ukuganiza kuti ungadzakhale mfumu yathu?+ Moti ukuona kuti ungadzatilamulire ife?”+ Kwa iwo, maloto amenewa ndi mawu akewa anakhala chifukwa chinanso chomudera.
8 Pamenepo abale akewo anamufunsa kuti: “Kodi iweyo ndithu ukuganiza kuti ungadzakhale mfumu yathu?+ Moti ukuona kuti ungadzatilamulire ife?”+ Kwa iwo, maloto amenewa ndi mawu akewa anakhala chifukwa chinanso chomudera.