-
1 Mafumu 20:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Pamene mfumu inali kudutsa, mneneriyo analankhula mofuula kwa mfumuyo kuti:+ “Ine mtumiki wanu ndinapita pakatikati pa nkhondo. Munthu wina yemwe anali kuchoka kunkhondoko anandisungitsa munthu n’kundiuza kuti, ‘Uyang’anire munthu uyu. Akangosowa, moyo wako+ ulowa m’malo mwa moyo wake,+ apo ayi ulipira siliva wolemera talente* imodzi.’+
-