21 Ndiyeno Yehova anamva fungo lokhazika mtima pansi,+ moti ananena mumtima+ mwake kuti: “Sindidzatembereranso nthaka+ chifukwa cha zochita za anthu, popeza maganizo+ a anthu amakhala oipa kuyambira pa ubwana wawo.+ Ndipo sindidzawononganso chilichonse monga ndachitiramu.+