Genesis 41:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Mwana woyambayo Yosefe anamutcha dzina lakuti Manase,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse, ndi nyumba yonse ya bambo anga.”+ Salimo 89:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mkono wamphamvu ndi wanu,+Dzanja lanu ndi lamphamvu,+Dzanja lanu lamanja ndi lokwezeka.+ Machitidwe 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipotu Davide sanakwere kumwamba,+ koma iye mwini anati, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+ Aefeso 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 imene waigwiritsa ntchito pa Khristu pamene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kumukhazika kudzanja lake lamanja+ m’malo akumwamba.+
51 Mwana woyambayo Yosefe anamutcha dzina lakuti Manase,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse, ndi nyumba yonse ya bambo anga.”+
34 Ndipotu Davide sanakwere kumwamba,+ koma iye mwini anati, ‘Yehova anauza Ambuye wanga kuti: “Khala kudzanja langa lamanja+
20 imene waigwiritsa ntchito pa Khristu pamene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kumukhazika kudzanja lake lamanja+ m’malo akumwamba.+