-
Yesaya 66:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 “Ndidzachita zinthu zazikulu pakati pawo monga chizindikiro.+ Opulumuka ena ndidzawatumiza ku mitundu ya anthu,+ ku Tarisi,+ ku Puli, ndi ku Ludi.+ Ndidzawatumiza kwa anthu odziwa kukoka uta ku Tubala ndi ku Yavani.+ Ndidzawatumiza kuzilumba zakutali,+ kwa anthu amene sanamve mbiri yanga kapena kuona ulemerero wanga.+ Iwo adzanenadi za ulemerero wanga pakati pa mitundu ya anthu.+
-