Salimo 104:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akasupewo amapereka madzi kwa zilombo zonse zakutchire.+Nthawi zonse mbidzi+ zimapha ludzu lawo mmenemo. Maliko 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero iye anakhala m’chipululumo masiku 40,+ akuyesedwa ndi Satana.+ M’chipululumo munalinso nyama zakutchire. Pambuyo pake, angelo anam’tumikira.+
11 Akasupewo amapereka madzi kwa zilombo zonse zakutchire.+Nthawi zonse mbidzi+ zimapha ludzu lawo mmenemo.
13 Chotero iye anakhala m’chipululumo masiku 40,+ akuyesedwa ndi Satana.+ M’chipululumo munalinso nyama zakutchire. Pambuyo pake, angelo anam’tumikira.+