Salimo 68:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Dzudzulani nyama yakutchire yokhala m’mabango,+ gulu la ng’ombe zamphongo,+Pamodzi ndi mitundu ya anthu imene ili ngati ana a ng’ombe amphongo, aliyense amene akupondaponda ndalama zasiliva.+Iye wabalalitsa mitundu ya anthu yokonda ndewu.+ Luka 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Wachita zamphamvu ndi dzanja lake,+ wabalalitsira kutali odzikweza m’zolinga za mitima yawo.+
30 Dzudzulani nyama yakutchire yokhala m’mabango,+ gulu la ng’ombe zamphongo,+Pamodzi ndi mitundu ya anthu imene ili ngati ana a ng’ombe amphongo, aliyense amene akupondaponda ndalama zasiliva.+Iye wabalalitsa mitundu ya anthu yokonda ndewu.+