Genesis 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye.
7 Ndiyeno Yehova anaonekera kwa Abulamu n’kumuuza kuti: “Ndidzapereka dziko ili+ kwa mbewu yako.”+ Pambuyo pake, iye anamanga pamalopo guwa lansembe la Yehova, yemwe anaonekera kwa iye.