-
2 Petulo 2:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Munthu wolungama ameneyo anali kuzunzika tsiku ndi tsiku ndi zimene anali kuona ndi kumva pamene anali kukhala pakati pawo, ndiponso chifukwa cha zochita zawo zosamvera malamulo.
-