Genesis 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiye chonde, unene kuti ndiwe mlongo wanga+ kuti zindiyendere bwino. Ukatero upulumutsa moyo wanga.”+ Aefeso 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Akazi agonjere+ amuna awo ngati mmene amagonjerera Ambuye,
13 Ndiye chonde, unene kuti ndiwe mlongo wanga+ kuti zindiyendere bwino. Ukatero upulumutsa moyo wanga.”+