Miyambo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mtima wa mwamuna wake* umamudalira, ndipo mwamunayo sasowa kalikonse.+ 1 Akorinto 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndiponso mwamuna sanalengedwere mkazi, koma mkazi analengedwera mwamuna.+ 1 Timoteyo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti Adamu ndiye anayamba kupangidwa, kenako Hava.+