Genesis 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+ Yesaya 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndi amene ndimanena za mapeto kuyambira pa chiyambi.+ Kuyambira kalekale, ndimanena za zinthu zimene sizinachitike.+ Ine ndiye amene ndimanena kuti, ‘Zolingalira zanga zidzachitikadi,+ ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+ Machitidwe 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma ngati ikuchokera kwa Mulungu,+ simungathe kuwaletsa.+ Mukaumirira mukhoza kupezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”+
24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+
10 Ine ndi amene ndimanena za mapeto kuyambira pa chiyambi.+ Kuyambira kalekale, ndimanena za zinthu zimene sizinachitike.+ Ine ndiye amene ndimanena kuti, ‘Zolingalira zanga zidzachitikadi,+ ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+
39 Koma ngati ikuchokera kwa Mulungu,+ simungathe kuwaletsa.+ Mukaumirira mukhoza kupezeka kuti mukulimbana ndi Mulungu.”+