Oweruza 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo fuko la Yuda linakwezeka mtunda, ndipo Yehova anapereka Akanani ndi Aperezi m’manja mwawo,+ mwakuti anagonjetsa amuna 10,000 ku Bezeki. Oweruza 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo Yehova Mulungu wa Aisiraeli anapereka Sihoni ndi anthu ake onse m’manja mwa Aisiraeli. Choncho anawagonjetsa ndi kutenga dziko lonse la Aamori okhala kumeneko.+
4 Pamenepo fuko la Yuda linakwezeka mtunda, ndipo Yehova anapereka Akanani ndi Aperezi m’manja mwawo,+ mwakuti anagonjetsa amuna 10,000 ku Bezeki.
21 Pamenepo Yehova Mulungu wa Aisiraeli anapereka Sihoni ndi anthu ake onse m’manja mwa Aisiraeli. Choncho anawagonjetsa ndi kutenga dziko lonse la Aamori okhala kumeneko.+