Ekisodo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano uza anthu kuti mwamuna aliyense ndi mkazi aliyense apemphe kwa mnzake zinthu zasiliva ndi zagolide.”+ Ekisodo 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+
2 Tsopano uza anthu kuti mwamuna aliyense ndi mkazi aliyense apemphe kwa mnzake zinthu zasiliva ndi zagolide.”+
35 Ndipo ana a Isiraeli anachita mogwirizana ndi mawu onse amene Mose anawauza, motero anapempha Aiguputo zinthu zasiliva, zagolide ndi zovala.+