Ekisodo 40:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno analowetsa tebulo+ m’chihema chokumanako, n’kuliika kumbali yakumpoto ya chihemacho, kunja kwa nsalu yotchinga. Ekisodo 40:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako analowetsa guwa lansembe lagolide+ m’chihema chokumanako, ndi kuliika patsogolo pa nsalu yotchinga, Aheberi 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti panamangidwa chipinda choyamba cha chihema.+ M’chipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo,+ ndi mitanda ya mkate woonetsedwa,+ ndipo chinali kutchedwa “Malo Oyera.”+
22 Ndiyeno analowetsa tebulo+ m’chihema chokumanako, n’kuliika kumbali yakumpoto ya chihemacho, kunja kwa nsalu yotchinga.
26 Kenako analowetsa guwa lansembe lagolide+ m’chihema chokumanako, ndi kuliika patsogolo pa nsalu yotchinga,
2 Pakuti panamangidwa chipinda choyamba cha chihema.+ M’chipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo,+ ndi mitanda ya mkate woonetsedwa,+ ndipo chinali kutchedwa “Malo Oyera.”+