Ekisodo 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako utenge zovala+ zija ndi kuveka Aroni. Umuveke mkanjo ndi malaya odula manja a mkati mwa efodi.* Umuvekenso efodi ndi chovala pachifuwa. Efodiyo um’mange bwino ndi lamba wake.+
5 Kenako utenge zovala+ zija ndi kuveka Aroni. Umuveke mkanjo ndi malaya odula manja a mkati mwa efodi.* Umuvekenso efodi ndi chovala pachifuwa. Efodiyo um’mange bwino ndi lamba wake.+