Ekisodo 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 mafuta a nyale,+ mafuta a basamu+ opangira mafuta odzozera,+ ndi zofukiza zonunkhira.+ Salimo 141:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+ Chivumbulutso 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Atatenga mpukutuwo, zamoyo zinayi ndi akulu 24 aja+ anagwada ndi kuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze woimbira+ ndi mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. Zofukizazo+ zikuimira mapemphero+ a oyera.
2 Pemphero langa likhale lokonzedwa ngati zofukiza+ pamaso panu,+Mapembedzero anga akhale ngati nsembe yambewu yamadzulo.+
8 Atatenga mpukutuwo, zamoyo zinayi ndi akulu 24 aja+ anagwada ndi kuwerama pamaso pa Mwanawankhosa. Aliyense wa iwo anali ndi zeze woimbira+ ndi mbale yagolide yodzaza ndi zofukiza. Zofukizazo+ zikuimira mapemphero+ a oyera.